(Download) "Kutaya Kusautsidwa Kupereka Nsembe ndi Kumwalira" by Dag Heward-Mills " Book PDF Kindle ePub Free

eBook details
- Title: Kutaya Kusautsidwa Kupereka Nsembe ndi Kumwalira
- Author : Dag Heward-Mills
- Release Date : January 22, 2019
- Genre: Christianity,Books,Religion & Spirituality,
- Pages : * pages
- Size : 766 KB
Description
Azibusa ali pa mpani pani wokondweretsa ndi kusangalatsa anthu awo ndi uthenga wabwino. Mpani pani wa anthu umenewu wapangitsa kusintha kwa mawu a Khristu kufikira mawu a mtanda akhalira kovuta kuzindikirika.
Lero, tikubwerera ku maziko a chilungamo cha Chikhristu choti tikuyenera “kutaya” kuti “tipeze” Khristu. Mphamvu izabwerera ku mpingo pamene tikulalikira kuti tipereke nsembe, kusautsidwa ndi kufa chifukwa cha Khristu. Mphamvu ya mawu a Khristu siingafufutidwe ndi wina aliyense posatengera kuchita bwino kapena kukhala wa mphamvu.